Oweruza 12:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo amuna a Efraimu analalikidwa, napita kumpoto; nati kwa Yefita, Wapitiriraoji kuthira nkhondo ana a Amoni, osatiitana ife timuke nawe? Tidzakutenthera nyumba yako ndimotopamtupako.

Oweruza 12

Oweruza 12:1-11