Oweruza 11:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo mzimu wa Yehova unamdzera Yefita, napitira iye ku Gileadi, ndi Manase, napitira ku Mizipa wa Gileadi, ndi kucokera ku Mizipa wa Gileadi anapitira kwa ana a Amoni.

Oweruza 11

Oweruza 11:28-32