Oweruza 11:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pokhala Israyeli m'Hesiboni ndi midzi yace, ndi m'Aroeri ndi midzi yace, ndi m'midzi yonse yokhala m'mphepete mwa Arinoni zaka mazana atatu; munalekeranji kulandanso nthawi ija?

Oweruza 11

Oweruza 11:25-30