Oweruza 10:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthu, akalonga a Gileadi, ananenana wina ndi mnzace, Ndaniyo adzayamba kulimbana ndi ana a Amoni? iye adzakhala mkuru wa onse okhala m'Gileadi.

Oweruza 10

Oweruza 10:16-18