Oweruza 1:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Aamori anakhumbanso kukhala ku phiri la Heresi, ku Ajaloni, ndi ku Saalibimu; koma dzanja la a m'nyumba ya Yosefe linawalaka, nakhala iwo akupereka msonkho.

Oweruza 1

Oweruza 1:27-36