Oweruza 1:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, m'mene anamdzera, anamkakamiza mwamuna wace kuti apemphe atate wace ampatse munda; natsika pa buru wace; ndipo Kalebe ananena naye, Ufunanji?

Oweruza 1

Oweruza 1:10-17