Obadiya 1:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsiku lija unaima padera, tsiku lija alendo anagwira ndende makamu ace, nalowa m'zipata zace acilendo, nacitira Yerusalemu maere, iwenso unakhala ngati mmodzi wa iwowa.

Obadiya 1

Obadiya 1:7-15