Nyimbo 8:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Madzi ambiri sangazimitse cikondi,Ngakhale mitsinje yodzala kucikokolola:Mwamuna akapereka katundu yense wa m'nyumba yace ngati sintho la cikondi,Akanyozedwa ndithu.

Nyimbo 8

Nyimbo 8:1-9