Ndinatsikira ku munda wa ntedza,Kukapenya msipu wa m'cigwa,Kukapenya ngati pamipesa paphuka,Ngati pamakangaza patuwa maluwa.