Nyimbo 4:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Idza nane kucokera ku Lebano, mkwatibwi,Kucokera nane ku Lebano:Unguza pamwamba pa Amana,Pa nsonga ya Seniri ndi Hermoni,Pa ngaka za mikango,Pa mapiri a anyalugwe.

Nyimbo 4

Nyimbo 4:6-16