Nyimbo 3:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndikulumbirirani, ana akazi inu a ku Yerusalemu,Pali mphoyo, ndi nswala ya kuthengo,Kuti musautse, ngakhale kugalamutsa cikondi,Mpaka cikafuna mwini.

Nyimbo 3

Nyimbo 3:1-11