Nyimbo 2:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndikulumbirirani, ana akazi inu a ku Yerusalemu,Pali mphoyo, ndi nswala za kuthengo,Kuti musautse, ngakhale kugalamutsa cikondi,Mpaka cikafuna mwini.

Nyimbo 2

Nyimbo 2:1-11