Numeri 9:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsiku lakhumi ndi cinai la mweziwo, madzulo, muziucita, pa nyengo yace yoikidwa; muucite monga mwa malemba ace onse, ndi maweruzo ace onse.

Numeri 9

Numeri 9:1-8