Numeri 9:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pokwera mtambo kucokera kucihema, utatero ana a Israyeli amayenda ulendo wao; ndipo pamalo pokhala mtambo, pamenepo ana a Israyeli amamanga mahema ao.

Numeri 9

Numeri 9:11-19