Numeri 8:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo atatero, Alevi analowa kucita Debito yao m'cihema cokomanako pamaso pa Aroni, ndi pamaso pa ana ace amuna; monga Yehova anauza Mose kunena za Alevi, momwemo anawacitira.

Numeri 8

Numeri 8:16-26