Numeri 7:59 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi nsembe yoyamika, ng'ombe ziwiri, nkhosa zamphongo zisanu, atonde asanu, ana a nkhosa asanu a caka cimodzi; ndico copereka ca Gamaliyeli mwana wa Pedazuri.

Numeri 7

Numeri 7:58-63