Numeri 6:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Asadzidetse ndi atate wace, kapena mai wace, mbale wace, kapena mlongo wace, akafa iwowa; popeza cowindira Mulungu wace ciri pamutu pace.

Numeri 6

Numeri 6:4-9