Numeri 6:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Mnaziriyo amete mutu wace wa kusala kwace pa khomo la cihema cokomanako, natenge tsitsi la pa mutu wace wa kusala, naliike pamoto wokhala pansi pa nsembe yoyamika.

Numeri 6

Numeri 6:11-21