Numeri 6:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo wansembe akonze imodzi nsembe yaucimo, ndi yina nsembe yopsereza, namtetezere popeza anacimwa nao mtembowo; ndipo apatulire mutu wace tsiku lomwelo.

Numeri 6

Numeri 6:3-20