Numeri 5:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ana a Israyeli anacita cotero, nawaturutsira kunja kwa cigono; monga Yehova adanena ndi Mose momwemo ana a Israyeli anacita.

Numeri 5

Numeri 5:1-7