Numeri 5:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kapena pamene mtima wansanje umgwira mwamuna, ndipo acitira mkazi wace nsanje; pamenepo aziika mkazi pamaso pa Yehova, ndipo wansembe amcitire cilamulo ici conse.

Numeri 5

Numeri 5:23-31