Numeri 5:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo ukamgwira mwamuna mtima wansanje, kuti acitire nsanje mkazi wace, popeza wadetsedwa; kapena ukamgwira mtima wansanje, kuti amcitire mkazi wace nsanje angakhale sanadetsedwa;

Numeri 5

Numeri 5:10-17