Numeri 4:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo atenge nsaru yamadzi, ndi kuphimba coikapo nyali younikira, ndi nyali zace, ndi mbano zace, ndi zaolera zace, ndi zotengera zace zonse za mafuta zogwira nazo nchito yace.

Numeri 4

Numeri 4:2-12