Numeri 4:45 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Amenewo ndiwo owerengedwa a mabanja a ana a Merari, amene Mose ndi Aroni anawawerenga monga mwa mau a Yehova mwa dzanja la Mose.

Numeri 4

Numeri 4:44-49