Numeri 4:41 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Amenewo ndiwo owerengedwa a mabanja a ana a Gerisoni, onse akutumikira m'cihema cokomanako, adawawerenga Mose ndi Aroni monga mwa mau a Yehova.

Numeri 4

Numeri 4:40-42