Numeri 4:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Awa ndi owerengedwa a mabanja a Akohati, onse akutumikira m'cihema cokomanako, amene Mose ndi Aroni anawawerenga monga mwa mau a Yehova mwa dzanja la Mose.

Numeri 4

Numeri 4:35-40