Numeri 4:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Natenge zipangizo zace zonse za utumiki, zimene atumikira nazo m'malo opatulika, nazimange m'nsaru yamadzi, ndi kuziphimba ndi cophimba ca zikopa za akatumbu, ndi kuziika paconyamulira.

Numeri 4

Numeri 4:10-22