Numeri 36:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pofika caka coliza ca ana a Israyeli adzaphatikiza colowa cao ku colowa ca pfuko limene akhalako; cotero adzacotsa colowa cao ku colowa ca pfuko la makolo athu.

Numeri 36

Numeri 36:1-7