Numeri 35:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

popeza wakupha munthu akadakhala m'mudzi wace wopulumukirako kufikira atafa mkulu wa ansembe; koma atafa mkulu wa ansembe wakupha munthuyo abwere ku dziko lace lace.

Numeri 35

Numeri 35:27-34