Numeri 33:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anacokera ku Mara, nayenda nafika ku Elimu, ku Elimu ndiko kuli akasupe khumi ndi awiri a madzi, ndi akanjedza makumi asanu ndi awiri; namanga iwo komweko.

Numeri 33

Numeri 33:1-17