Numeri 33:38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Aroni wansembe anakwera m'phiri la Hori pa mau a Yehova, nafa komweko, ataturuka ana a Israyeli m'dziko la Aigupto zaka makumi anai, mwezi wacisanu, tsiku loyamba la mwezi.

Numeri 33

Numeri 33:36-42