Numeri 33:27-29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

27. Nacokera ku Tahata, nayenda namanga m'Tara.

28. Nacokera ku Tara, nayenda namanga m'Mitika.

29. Nacokera ku Mitika, nayenda namanga m'Hasimona.

Numeri 33