Numeri 32:35-37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

35. Ataroti Sofani, Yazeri, ndi Yogebeha;

36. ndi Beti Nimira, ndi Beti Harani: midzi ya m'malinga, ndi makola a zoweta.

37. Ndipo ana a Rubeni anamanga Hesiboni, ndi Eleyali, ndi Kiriyataimu;

Numeri 32