Numeri 32:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ana a Gadi ndi ana a Rubeni anayankha, nati, Monga Yehova anati kwa anyamata anu momwemo tidzacita.

Numeri 32

Numeri 32:24-32