Numeri 31:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ana a Israyeli anagwira akazi a Amidyani, ndi ana ang'ono, nafunkha ng'ombe zao zonse, ndi zoweta zao zonse, ndi cuma cao conse.

Numeri 31

Numeri 31:7-18