Numeri 31:47 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

mwa gawolo la ana a Israyeli Mose anatenga munthu mmodzi mwa makumi asanu, ndi zoweta momwemo, nazipereka kwa Alevi, akusunga udikiro wa kacisi wa Yehova; monga Yehova adamuuza Mose.

Numeri 31

Numeri 31:45-50