Numeri 31:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo limodzi la magawo awiri, ndilo gawo la iwo adaturuka kunkhondo, linafikira nkhosa zikwi mazana atatu mphambu makumi atatu kudza zisanu ndi ziwiri mphambu mazana asanu.

Numeri 31

Numeri 31:35-40