Numeri 31:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo zakunkhondo, zotsalira zofunkha zonse adazifunkha ankhondowa, ndizo nkhosa zikwi mazana asanu ndi limodzi mphambu zikwi makumi asanu ndi awiri kudza zisanu,

Numeri 31

Numeri 31:24-34