Numeri 31:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose ananena ndi anthu, nati, Adzikonzere ena mwa inu zida za nkhondo, alimbane nao Amidyani, kuwabwezera Amidyani cilango ca Yehova.

Numeri 31

Numeri 31:1-6