Numeri 30:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mkazi akacitira Yehova cowinda, nakadzimanga naco codziletsa, pokhala ali m'nyumba ya atate wace, m'unamwali;

Numeri 30

Numeri 30:1-7