Numeri 3:50 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

analandira ndaramazo kwa oyamba kubadwa a ana a Israyeli; masekeli cikwi cimodzi mphambu mazana atatu kudza makumi asanu ndi limodzi mphambu asanu, kuyesa sekeli wa malo opatulika.

Numeri 3

Numeri 3:42-51