Numeri 3:39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Owerengedwa onse a Alevi, adawawerenga Mose ndi Aroni, powauza Yehova, monga mwa mabanja ao, amuna onse kuyambira a mwezi umodzi ndi mphambu, ndiwo zikwi makumi awiri mphambu ziwiri.

Numeri 3

Numeri 3:31-42