Numeri 3:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi kalonga wa nyumba ya makolo ya mabanja a Merari ndiye Zuriyeli mwana wa Abiyaili; azimanga mahema ao pa mbali ya kacisi ya kumpoto.

Numeri 3

Numeri 3:27-44