Numeri 3:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Powawerenga amuna onse, kuyambira a mwezi umodzi ndi mphambu ndiwo zikwi zisanu ndi zitatu mphambu mazana asanu ndi limodzi, akusunga udikiro wa pa malo opatulika.

Numeri 3

Numeri 3:18-31