Numeri 3:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo taonani, Ine ndatenga Alevi kuwacotsa pakati pa ana a Israyeli m'malo mwa ana ovamba onse, oyamba kubadwa mwa ana a Israyeli; ndipo Aleviwo ndi anga.

Numeri 3

Numeri 3:6-13