Numeri 29:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi nsembe yace yaufa, ndi nsembe zace zothira za ng'ombe, za nkhosa zamphongo, ndi za ana a nkhosa monga mwa kuwerenga kwace, ndi kutsata lemba lace;

Numeri 29

Numeri 29:15-25