Numeri 28:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momwemonso tsiku la zipatso zoyamba, pobwera nayo nsembe ya ufa watsopano kwa Yehova, m'madyerero anu a masabata, muzikhala nako kusonkhana kopatulika; musamacita nchito ya masiku ena.

Numeri 28

Numeri 28:17-28