Numeri 28:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Ndipo Yehova ananena ndi Mose, nati, Uza ana a Israyeli, nuti nao, Muzisamalira kubwera naco kwa Ine copereka canga