Numeri 26:48 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ana amuna a Nafitali monga mwa mabanja ao ndiwo: Yazeli, ndiye kholo la banja la Ayazeli; Guni, ndiye kholo la banja la Aguni;

Numeri 26

Numeri 26:42-51