Numeri 26:44 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ana amuna a Aseri monga mwa mabanja ao ndiwo: Yimna, ndiye kholo la banja la Ayimna; Yisivi, ndiye kholo la banja la Ayisivi; Beriya, ndiye kholo la banja la Aberiya.

Numeri 26

Numeri 26:42-45